by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Islam, Misconceptions
Kuchokera mu Minhaajul Qaaswideen fi Fadhlil Khulafaai Rraashideen page 187, tidziwa kuti nawo ma Khawaarij amadana ndi ena mwa ma Swahaba. Khawaarij ndigulu la anthu omwe anali limodzi ndi Ali radhia Allah anhu pa nkhondo zake, koma anamutuluka ndikumuwukira pamene...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fatawa, Featured, Fiqh, Islam, Islamic Manners, Marriage, Misconceptions
خـــاتَمُ الخِـــطْبَةِ ENGAGEMENT (WEDDING) RING(Sheikh Naasiru Ddeen Al-Albaani) Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa uyo yemwe Allah anamutumiza kuti adzakwaniritse makhalidwe abwino. Pali zichitochito zina...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Islam, Misconceptions, Role Models
“Kodi ‘Uthman Radhia Allah Anhu Atamwalira Anaikidwa Kuti?” ‘Uthman radhia Allah anhu atamwalira anasambitsidwa ndi kuvekedwa, ndipo kenako ananyamulidwa ndigulu la antchito ake, ndipo anapempheretsa janaza yake Swahaba Jubayru bun Mut’im, ma...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Fiqh, Misconceptions, Salaat
Taraweh ndi swalaat yausiku yomwe timaswali mmwezi wa Ramadhan, pokwaniritsa Sunnah ya Mtumiki salla Allah laaih wasallam yomwe sanali kuisiya. Ndipo swalaat imeneyi imatheka kuswalidwa pa jamaah kapena pawekha kunyumba, monganso mmene Mtumiki anali kuchitira....
by Admin | Sep 3, 2021 | Fiqh, Islam, Misconceptions, Salaat
Anthu ambiri akamaliza swalah za faradh ndikumaliza kupanga ma Adhikaar, amanyamula manja awo ndikuyamba kupanga Dua pagulu kapena payekhapayekha aliyense. Ndipo pali gulu la anthu ena omwe samapanga, koma amati akamaliza kupanga ma adhkaar basi amatuluka, poti ma dua...
by Admin | Sep 3, 2021 | Featured, Fiqh, Misconceptions
Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Yemwe ananena kuti: Watukuka ndi kudalitsika (Allah) Amene m’manja Mwake muli ufumu (wochita chilichonse pazolengedwa zonse); ndipo Iye ali ndi mphamvu yokwanira pachilichonse. Amene adalenga imfa ndi moyo kuti akuyeseni (mayeso) ndani...
Your Comments