Learn Islam

Kuvala Hijaab ndi Zolinga zake Mchisilamu

بسمِ الله الرحمن الرحيم KUVALA HIJAB NDI ZOLINGA ZAKE MCHISILAMU Uwu ndi uthenga kwazichemwali athu a Chisilamu.Alhamdulilah kuti Masiku ano Hijab ili paliponse limodzi ndi kutsogola kwa ma company opanga Zovala makamaka mikanjo yazimayi.kuli Mitundu Yochuluka ya...

Kumasulira Khutbah

KODI NDIZOLOLEDWA KUMASULIRA KHUTBAH YA JUM'AH MUCHIYANKHULO CHINA ZITAKHALA KUTI ANTHU OMVETSERA SAKUVA CHIARABU? Nkhaniyi anthu amasiyana zokamba zenizeni chifukwa choti nthawi ya Mtumiki kunalibe kumasulira, komanso panalibe chifukwa chomasulira khutbah poti...

Dua Yamphamvu

Kuchokera kwa Ibn Abbas radhia Allah anhu: Mtumiki wa Allah (ﷺ) amatuluka mnyumba mwa mkazi wake, Juwayriyyah - dzina lake koyamba linali Barrah, koma anasintha - pamene Mtumiki anatuluka, Juwayriyyah anali pamalo opemphelera mpaka pamene anabwelera. Mtumiki...

Kudya Dothi

Kudya dothi ndi chizolowezi chosafunikira chomwe chimachitika ndi azimai ngakhalenso ana ena. Nthawi zina chimakhala chikhalidwe chotengera, pomwe nthawi zina zikhonza kubwera kuchokera mu condition inayake yamthupi, monga kusowa kwa michere ina makamaka iron....

Your donation is higly appreciated. If you wish to help, click below for contact details

Zolembedwa zonse za muwebusayitiyi ndizotetezedwa ndi alembi. Pamene mukopera kuti mugawe uthenga kwa ena, onesetsani kuti mwakoperanso link ya ulalikiwo, ndipo musasinthe kalikonse mkati mwaulaliki.