‘Uthmaan bun ‘Afaan (Dhu Al-Nurain)

Mbiri ya ‘Uthmaan bun ‘Affaan mwachidule Alongosolereni ana anu achichepere nkhani zimenezi Uthman bun Affaan radhia Allah anhu anabadwa patadutsa zaka 7 chibadwire Mtumiki salla Allah alaih wasalaam. Iye anali ochokera mu nthambi ya fuko la Quraysh...

‘Umar bun Al-Khattwaab (Al-Faaruq)

Mbiri ya Umar bun Al-Khattwaab mwachidule Alongosolereni ana anu achichepere nkhani zimenezi Umar bun Al Khattaab radhia Allah anhu anali mmodzi mwa ma Khalifa amphamvu komanso opambana, ochokera m’banja la Bani ‘Adiy, fuko la Quraysh ku Makkah. Anali...

‘Abdullah bun Abi Quḥafah (Abu Bakr Al-Siddiq)

Mbiri ya Abu Bakr Al Siddiq mwachidule Alongosolereni ana anu achichepere nkhani zimenezi Abu Bakr anabadwira ku Makkah kuchokera mu fuko chi Quraysh, la Banu Taimi. Dzina lake lenileni linali Abdul Ka’ba (Kapolo wa Ka’ba) ndipo dzina loti Abu Bakr...