by Admin | Dec 16, 2020 | Featured, Kuunikira
بسمِ الله الرحمن الرحيم KUVALA HIJAB NDI ZOLINGA ZAKE MCHISILAMU Uwu ndi uthenga kwazichemwali athu a Chisilamu.Alhamdulilah kuti Masiku ano Hijab ili paliponse limodzi ndi kutsogola kwa ma company opanga Zovala makamaka mikanjo yazimayi.kuli Mitundu Yochuluka ya...
by Admin | Dec 10, 2020 | Fatawa, Featured, Fiqh, Salaat
KODI NDIZOLOLEDWA KUMASULIRA KHUTBAH YA JUM’AH MUCHIYANKHULO CHINA ZITAKHALA KUTI ANTHU OMVETSERA SAKUVA CHIARABU? Nkhaniyi anthu amasiyana zokamba zenizeni chifukwa choti nthawi ya Mtumiki kunalibe kumasulira, komanso panalibe chifukwa chomasulira khutbah poti...
by Admin | Dec 10, 2020 | Featured, Islam
Kuchokera kwa Ibn Abbas radhia Allah anhu: Mtumiki wa Allah (ﷺ) amatuluka mnyumba mwa mkazi wake, Juwayriyyah – dzina lake koyamba linali Barrah, koma anasintha – pamene Mtumiki anatuluka, Juwayriyyah anali pamalo opemphelera mpaka pamene anabwelera....
by Admin | Aug 5, 2020 | Fatawa, Featured
Kudya dothi ndi chizolowezi chosafunikira chomwe chimachitika ndi azimai ngakhalenso ana ena. Nthawi zina chimakhala chikhalidwe chotengera, pomwe nthawi zina zikhonza kubwera kuchokera mu condition inayake yamthupi, monga kusowa kwa michere ina makamaka iron....
by Admin | Jul 27, 2020 | Featured, Islam
Kodi Experiment (Kuyesera) ili ndi gawo muntchito ya Ruqya? Experiment imachitika mu makhwala (akuchipatala kapena azisamba). Udokotala ngakhalenso using’anga zimachokera mma experiment pofuna kupeza mankhwala anthenda inayake. Pomwe Ruqya, Msilamu akuyenera...
Your Comments