Salaat Laylatul Qadr

Swalaat Laylatul Qadr…?? Kuchokera mu Sahih Al Bukhari ndi Muslim, Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam anati: “Yemwe waima kupemphera usiku wa Lailatul Qadr mwa chikhulupiliro (Imaan) komanso moyembekeza malipiro, amakhululukidwa machimo ake”...

Kupemphera Usiku

Allah Ta’la amayandikira (ndi ulemelero wake) usiku uliwonse pa thambo la dziko lapansi, ndipo amaitana: “kodi alipo yemwe akundipempha ndimuyankhe? nanga alipo yemwe akupempha chikhululuko ndimukhululukire? kodi alipo yemwe akufuna kulapa machimo ake...
Distinguishing Features of Salaat

Distinguishing Features of Salaat

What is Salaat Salaat is one of the forms of worship (Ibaadah) which commences with Takbiratul Ihraam (saying Allahu Akbar) and ends with Tasleem (Saying Assalaam alaikum warahmatullah) It is an obligatory worship to all Muslims. It is the second of the five pillars...
Nthawi za Mapemphero

Nthawi za Mapemphero

Ambiri masiku ano amasokonezeka nthawi ya swalat yomwe anaphunzitsa Mtumiki salla Alaih waallam, ndi  wotchi makamaka akapita dziko lina. Ena anati “mzikiti womwe timaswali kuno ndi wa Mashia chifukwa akumachita adhaan ya Dhuhr past 1, pomwe ku Malawi timaswali...
Swalaat ya pa Mpando

Swalaat ya pa Mpando

Kukhala pa Mpando Poswali (Munthu yemwe akuloledwa kuswaali atakhala pampando akhale otani) 1. Akhale kuti akulephera kuimilira pa Swalaat Kuphatikiza kulephera kupanga rukuu’ ndi sajda molongosoka. Choncho aswali chokhala. Monga mmene Mtumiki salla Allah alaih...
Kuswali Pamene Khatwib ali pa Minbar

Kuswali Pamene Khatwib ali pa Minbar

بسم الله الرحمن الرحيم من كتاب/ الكلمات النافعة في الأخطاء الشائعة صـ330 75 خطأ في صلاة الجمعة Zolakwika 75 za Tsiku la Jum’ah No. 8 Kusiya kuswali Tahiyyatal Masjid ••••••• Tahiyyatul Masjid ndi ma rakaat awiri omwe munthu amayenera kuswali akangolowa munzikiti...