by Hamdan Zefa | Mar 6, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza lachinayi: “Mitala imachepetsa ma Rizq” Lina mwa maina a Allaah ndi Ar-Razzaaq (Wopereka ma Rizq). Tikamakamba za ma Rizq, tikukamba chirichonse chimene munthu amapeza pano pa dziko lapansi ndipo Mwini ma rizq amenewa ndi Allaah osati ife anthu....
by Hamdan Zefa | Mar 6, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza lachitatu: “Mitala imayambitsa matenda” Nkhani ya mitala idazunguliridwa ndi zokamba zambiri zomwe sizili zolondola. Kwa ena mwa akazi amene mwamuna wawo wagwidwa akugonana ndi mkazi wina, iwo samakhumbanso kuti akhudzidwe (akhale limodzi ndi mwamuna...
by Hamdan Zefa | Mar 6, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Ibn Qudaamah mu Al-Mughniy, (vol. 8, tsamba 151) adati: وَقَدْ اشْتُهِرَ بينَ النَّاس وجودُ عَقْدِ الرَّجُلِ عن امرأتِه حينَ يَتزوَّجُها. فلا يَقْدِرُ على إتْيانِها، وحَلُّ عَقْدِه، فيَقْدِرُ عليها بعدَ عَجْزِه عنها، حتى صار مُتواتِرًا لا يُمْكِنُ جَحْدُه. ورُوِىَ من...
by Hamdan Zefa | Mar 5, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza lachiwiri (2/1) “Mitala imayambitsa ufiti” Akazi ena amaopa kuvomera kukhala mkazi wachiwiri, wachitatu kapena wachinayi chifukwa choti adamva zoti mkazi woyamba amachita matsenga kapena ufiti kuti awapatse mavuto akazi amene mwamuna wake...
by Hamdan Zefa | Mar 4, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza loyamba: “Akazi pa mitala amakhala m’nyumba imodzi” Anthu ena amaganiza kuti mitala ikutanthawuza kuti mwamuna atenge akazi awiri ndikumakhala nawo m’nyumba imodzi, komanso kuti mikangano imene ingakhalepo pakati pa akaziwa itha...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fatawa, Featured, Fiqh, Islam, Islamic Manners, Marriage, Misconceptions
خـــاتَمُ الخِـــطْبَةِ ENGAGEMENT (WEDDING) RING(Sheikh Naasiru Ddeen Al-Albaani) Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa uyo yemwe Allah anamutumiza kuti adzakwaniritse makhalidwe abwino. Pali zichitochito zina...
Your Comments