by Admin | May 25, 2022 | Featured, Role Models, Shia
Ma Shia amamunena Mai wathu Wolemekezeka Aisha radhia Allahu anha kuti ndi munaafiq, komanso ndi wachimasomaso. Kuwonjezera pamenepo, m’mabuku mwawo akamamutchula mkazi wa Mtumiki aliyense amamutchula kuti Ummul Mu’mineena mkazi wa Mtumiki alaiha Ssalaam,...
by Admin | May 24, 2022 | Featured, Islam, Prophets
A TURNING POINT IN THE HISTORY OF ISLAM. Abdulkarim Shuaib May 20, 2022 02:56AM (Source: Book of Seerah ibn Hisham and Arab news 2012 religion article) The incident of Hudaibiyah reserves in history a significant phase of Islam when Muslims got an opportunity to...
by Kuunikira | May 24, 2022 | Fatawa, Featured, Kuunikira, Marriage, Sunnah
Tisaiwale kukumbukira kuti Kusangalala tsiku la Nikkah, sikuti Ndi chikakamizo ayi, koma kuti ndi Sunnah, chifukwa Anthu amazikakamiza ndikupanikizika Poona kuti afune asafune akuyenera kuchititsa Chisangalalo cha Nikkah yawo,dziwani kuti Kumangitsa Nikkah ndi chinthu...
by Kuunikira | May 24, 2022 | Featured, Kuunikira
Pakukhala kuti Chisilamu chidaunikira mbali zonse za umoyo, Mu Qur’an ndi Mahadith (zoyankhula za mtumiki). Ndipo masahabah Adagwira ntchito yotamandika yotulutsa khokwe za maphunziro kuchokera mu Qur’an ndi Mahadith, pambuyo pawo padabweraso Ma Imam ndi...
Your Comments