Al Bayyinah – Tiwadziwe ma Shia

Kutamandidwa konse ndi kwa Allaah, Wapamwambamwamba, Yemwe alibe wothandizana naye mu Ufumu Wake, Yemwe ali m’Modzi, Yemwe ali Wakutha kuchita chili chonse ndipo kwa Iye ndi komwe kuli Chiongoko. Mtendere ndi madalitso zipite kwa Mtumiki Muhammad (ﷺ), aku banja ake...

Zina mwa Zabodza Mmabuku a Shi’ah

Bodza la Mashia lonena kuti pali umboni woti Ali radhia Allahu anhu ndi Khalifa woyamba osati Abu Bakr radhia Allahu anhu  185- حتى لا ننخدع حقيقة الشيعة Pamene ma Swahaba wonse anagwirizana za utsogoleri komanso ulowammalo wa Abu Bakr, ‘Umar, ‘Uthman, kenako Ali...

Shahaadah ya Mashia

Idris Al Maghribi anali Msilamu waku Morocco ndipo atakumana ndi da’wah ya ma Shia, anaganiza zosiya Chisilamu nkulowa Shia. Pa mwambo wa “kusinguka” (kutuluka mu chipembedzo china kuliwa mu chipembedzi china), pamene Yaasir Al Habib yemwe ndi mmodzi...

Zina mwa Zikhulupiliro za Mashia

1. Chiphunzitso cha chi Shia chimanena kuti “Aah” ndilimodzi mwa maina a Allah. Umboni: Ma’anil Akhbaar, chitabu cholembedwa ndi Al Qummi, page 304: Onani chithunzi 2. Ma Shia amakhulupilira kuti Abu Talib (Malume a Mtumiki), Abdullah ndi Aaminah (Makolo a...

Ahlu Bayt…

HUSAIN .. MADAD YA HUSAIN .. YA HUSAIN !! Nchifukwa chani ma Shia amatamanda ndi kulemekeza Husain (رضي الله عنه) yekha ndi kusiya ana ena onse a Ali (رضي الله عنه)? Kodi munayamba mwadzifunsapo funso limeneli? Nanga nkhani imeneyi inayamba yakudabwitsanipo?...