Ma Khawaarij

Ndilandireni nonse, pamene tikuyamba program yachiwiri pambuyo pakumaliza pakumaliza program yoyamba yomwe inali Mgwirizano wa pakati pa Munthu ndi Majinn, ndipo mmenemo tafotokoza mmene ubalewu umachitikira, mavuto amene ubalewu umabweretsa kwa munthu, mmene...

Chiyambi cha Ijtimaa’

Ijtimaa’ ndi kusonkhana kwa Asilamu kumene kumakhonzedwa ndi mabungwe a Chisilamu mogwirizana ndi Asilamu. Tikabwelera pachiyambi penipeni, tikupeza kuti ijtimaa’ inayamba ngati gawo limodzi lofunikra mu zochitika za Jamaat Tablighi padziko lonse, chifukwa...

Death of a Believer and a Non-believer

From the Book: Sahih Al Bukhari In the Name of Allah, The Beneficent, The Merciful Upon the authority of al-Bara’ ibn `Aazib who said: We went out with the Prophet (salla Allahu alaihi wa sallam) to a burial of a man from the Ansar (original inhabitants of...

Malangizo kwa Atsogoleri a Jihaad

Malangizo a Mtumiki salla Allah alaih wasallam kwa Atsogoleri a magulu a nkhondo: كانَ رَسولُ اللهِ صَلَّى اللَّهُ عليه وَسَلَّمَ إذَا أَمَّرَ أَمِيرًا علَى جَيْشٍ، أَوْ سَرِيَّةٍ، أَوْصَاهُ في خَاصَّتِهِ بتَقْوَى اللهِ، وَمَن معهُ مِنَ المُسْلِمِينَ خَيْرًا، ثُمَّ...

Kuipitsa Mbiri ya Usama bin Laden??

Funso: “Kodi nchifukwa chani mu ulaliki wa ma Khawaarij munasankha  kupereka chitsanzo nkhani ya Usama? mesa anali Msilamu? simukuona kuti anthu adziwona ngati mukumufukula zinsinsi zake kapenanso kumuweruza komans kuipitsa mbiiri yake? Komanso ambiri...