Kuwerenga Zitabu za Bid’ah

Kuwerenga Zitabu za Bid’ah

Kodi zoona ndi ziti pa nkhani ya kuwerenga zitabu za bid’ah komanso kumvera ma audio a ma Sheikh a bid’ah? Sizololedwa kwa munthu oyamba kumene kuphunzira, kapena yemwe sakuzindikira mokwanira; kuwerenga zitabu za bid’ah (zitabu zomwe zikukamba...
Oyenera Kupanga Da’wah

Oyenera Kupanga Da’wah

Anthu ena amaganiza kuti Da’wah (kuitanira kwa Allah) palibe yemwe angapange kupatula ma ulamaa okhaokha, ndipo omwe akuphunzira kwa ma Ulamaawo sakukakamizidwa kupanga Da’wah. Mutithandiza bwanji pa zimenezi?    Sikuti ndi maganizo chabe, koma ndizoona....
Bwalo la Fataawa

Bwalo la Fataawa

Kutulutsa zinthu za mu Mzikiti Sizololedwa kutulutsa zinthu za mu mzikiti kukadzigwiritsira ntchito malo ena osakhala munzikiti momwemo. Kubwereka mkeka, kapena Qur’an kaya mabuku aliwonse komanso china chirichonse chomwe chinaikidwa mu mzikiti kuti...
Zoletsedwa mu Nasheed

Zoletsedwa mu Nasheed

Kodi kuimba ma Nasheed ndikololedwa? Allah atipatse kuzindikira ********************** Ma nasheed omwe akuimbidwa mzaka zathu zino, ambiri ndi oletsedwa chifukwa akupezeka kunja kwa malamulo (ma condition) a nyimbo zololedwa omwe anabwera kale. Nasheed ndi yololedwa...
Dzina lake ndi “Mashaallah”

Dzina lake ndi “Mashaallah”

Funso: Abale anga okondedwa Mchipembedzo ndifunse nawo; kodi mwana ndibwino kumpatsa dzina lakuti “Mashaallah”? Ena akuti ndi zotheka chifukwa pali monga “Shukuran”, kuchokera ku Shukru-Llaah”, choncho “Mashaa-Allah”...
Nyimbo Mchisilamu

Nyimbo Mchisilamu

Kuchokera mu buku: “Ighaathatu Llahafaan min Maswaaid Shaytan” Lolembedwa ndi Ibn AlQayyim AlJawziy Nkhani ya nyimbo inali yomveka kalekale pamene kunalibe zomwe zikuchitika masiku ano. Ngakhale zili zomveka kuti nyimbo zogwiritsa ntchito zida ndi haraam,...