Kuchulukitsa Kulumbira Poyankhula

Pali anthu ena anazolowera kulumbira m’Dzina la Allah, mwachitsanzo kunena kuti “Wallahi…”, ndipo amachitenga kukhala chizolowezi chawo pakuyankhula kulikonse, zofunikira ngakhale zosafunikira. Chizolowezi choterechi ndicholakwika kwambiri....

Chisilamu ndi Dziko

Panopa dziko likuyenda chonchi:Yemwe amatsata za dziko akutengedwa kuti ndi otsogola chifukwa zikubwera mwatsopano. Ndiye otereyo kalikonse ka mu deen akumakachita mwa fashion malinga ndi mmene dziko likuyendera.  Yemwe amagwiritsa imaan yake molimba potsatira...

Al Mu’aidiyyu

Kulibwino kumangomva mbiri ya Al Mu’ayidiyy, kusiyana ndikumuwona تسمع عن المعيدي خير من أن تراه Umenewu ndi mwambi wa kalekale pakati pa ma Arabs munthawi ya umbuli Mtumiki asanabadwe. Ndipo anayankhula Al Nu’man bun Al Mundhir (yemwe anali mfumu pa...

Malangizo kwa Sheikh

Kodi ndi njira yanji yomwe ophunzira angalangizire Sheikh wake? Zomwe zili zoyenera ndi opposite; Sheikh ndi yemwe akuyenera kulangiza ophunzira wake, chifukwa iyeyo ndi amene ali ozindikira zinthu komanso odziwa kuposa ophunzirayo. Ophunzira nthawi zonse amakhala...

Kulemekeza ma Sheikh

Ma Ulamaa (anthu ozindikira komanso amaphunzitsa za deen ya Chisilamu), ndi anthu olemekezeka pamaso pa Allah chifukwa choti iwo ndi Alowammalo a Aneneri, ndi atsogoleri oyenera kuwalemekeza kuposa mtsogoleri wa dziko chifukwa akutitsogolera ku moyo wosatha....
Mkazi Kuvala Buluku

Mkazi Kuvala Buluku

“Ndi zoletsedwa mu Chisilamu mkazi kuvala buluku (thalauza) lothina ndikuonetsa mmene thupi lake liliri. Ndipo chilango chake ndi choopsa zedi chifukwa mchitidwe umenewu umafalitsa machimo pa dziko.” Darul Iftail Misriy Allah anaika ndondomeko ya momwe...