Kusala pa 15 Sha’baan

Kodi ndichiphunzitso cha Mtumiki kusala kwa tsiku la 15 Sha’baan? Hadith yomwe yabwera polimbikitsa swalaat ndi kusala komanso kuchita ibaada yosiyanasiyana pa 15 Sha’baan, siili mugulu la ma Hadith ofooka (a dhwaeef) koma ili mugulu la ma Hadith opeka komanso abodza...

Yakwanira Imfa Kukhala Mlaliki

Kodi n’chifukwa chani ma Sheikh amalalikira pamaliro ndi kumanda pomwe imfayo payokha ndi mlaliki? Tibwelere kaye mbuyo pang’ono, makamaka pa mawu oti: كَفَى بِالمَوْتِ وَاعِظًا “Yakwanira imfa kukhala mlaliki” Mawu amenewa ambiri amanena kuti ndi Hadith ya...

Kugawidwa Patatu kwa Mwezi wa Ramadhan

Kuchokera m’mawu omwe anthu amati ndi ochokera kwa Mtumiki salla Allah alaih wasallam, عن أبي هريرة قال: قال رسول الله ﷺ : أول شهر رمضان رحمة، وأوسطه مغفرة، وآخره عتق من النار. منكر، روه الديلمي Nkhani inachokera kwa Abi Hurairah radhia Allah anhu, anati:...