by Hamdan Zefa | Mar 4, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza loyamba: “Akazi pa mitala amakhala m’nyumba imodzi” Anthu ena amaganiza kuti mitala ikutanthawuza kuti mwamuna atenge akazi awiri ndikumakhala nawo m’nyumba imodzi, komanso kuti mikangano imene ingakhalepo pakati pa akaziwa itha...
by Admin | Feb 27, 2022 | Featured, Islam, Sunnah
Kodi n’chifukwa chani ma Sheikh amalalikira pamaliro ndi kumanda pomwe imfayo payokha ndi mlaliki? Tibwelere kaye mbuyo pang’ono, makamaka pa mawu oti: كَفَى بِالمَوْتِ وَاعِظًا “Yakwanira imfa kukhala mlaliki” Mawu amenewa ambiri amanena kuti ndi Hadith ya...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fasting, Featured, Fiqh, Islam, Sunnah
Kuchokera m’mawu omwe anthu amati ndi ochokera kwa Mtumiki salla Allah alaih wasallam, عن أبي هريرة قال: قال رسول الله ﷺ : أول شهر رمضان رحمة، وأوسطه مغفرة، وآخره عتق من النار. منكر، روه الديلمي Nkhani inachokera kwa Abi Hurairah radhia Allah anhu, anati:...
by Admin | May 7, 2020 | Salaat, Sunnah
Allah Ta’la amayandikira (ndi ulemelero wake) usiku uliwonse pa thambo la dziko lapansi, ndipo amaitana: “kodi alipo yemwe akundipempha ndimuyankhe? nanga alipo yemwe akupempha chikhululuko ndimukhululukire? kodi alipo yemwe akufuna kulapa machimo ake...
by Admin | Feb 16, 2020 | Featured, Sunnah
Pali ma hadith omwe anapekedwa nalembedwa mu buku kuti tidziwerenga poikira umboni kuti kuwerenga Qur’an ku Manda ndi Sunnah. Ma hadith amenewa ndi osafunika kuti tidziwagwiritsa ntchito tikawaona. Chifukwa ndi ma hadith oipa omwe amanamizira Mtumiki salla Allah...
by Admin | Feb 11, 2020 | Featured, Fiqh, Sunnah
GAWO LACHIWIRI Imodzi mwa nkhani zovuta kudzimvesetsa chifukwa cha kuchepekedwa kwa maphunziroku ndi yomwe ndikufuna kulongosola lero…ndipo pankhaniyi ndakhala ndikuona ma sheikh omwe akhala akuyesetsa kuwalongosolera anthu, akunyozedwa poyankhuliridwa...
Your Comments