Tiyidziwe Masjid Al Aqsa Yeniyeni

Ndizofunika Kwa Msilamu Aliyense Kudziwa Kusiyana Kwa Masjidul Aqsa Ndi Masjid Qubbat Assakharah. Kuyambira kalekale kwambiri, Masjidul Aqsa ku Palestine yakhala ikukumana ndi zipsinjo zambiri kuchokera kwa adani a Chisilamu omwe safuna kuona Chisilamu chikufalikira...

Tarweh ili ndi ma Rakaah Angati?

Taraweh ndi swalaat yausiku yomwe timaswali mmwezi wa Ramadhan, pokwaniritsa Sunnah ya Mtumiki salla Allah laaih wasallam yomwe sanali kuisiya. Ndipo swalaat imeneyi imatheka kuswalidwa pa jamaah kapena pawekha kunyumba, monganso mmene Mtumiki anali kuchitira....

Du’a Pambuyo pa Swalaat za Faradh

Anthu ambiri akamaliza swalah za faradh ndikumaliza kupanga ma Adhikaar, amanyamula manja awo ndikuyamba kupanga Dua pagulu kapena payekhapayekha aliyense. Ndipo pali gulu la anthu ena omwe samapanga, koma amati akamaliza kupanga ma adhkaar basi amatuluka, poti ma dua...

Kukhonzekera Mwezi wa Ramadhan

Kuyambikidwa konse nkwa Allah Mwini zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa Mtumiki wake wolemekezeka. Kodi tikhonzekere motani mwezi wa Ramadhan? Pamene tili pa chitseko cha mwezi wa Ramadhan, aliyense mwa ife akuyenera kuti akudziwa komwe akupita...

Mitala M’chisilamu

Mitala mu Chisilamu si LAMULO LOKAKAMIZIDWA, koma ndi chilolezo kwa yemwe wafuna. Allah Ta’la analoleza mitala mu Surat Al Nisaai Aayah #3. Nkhani ya mitala imavuta mbali zonse; kwa mwamuna ndi kwa mkazi komwe, chifukwa cha kusatsatira ndondomeko komanso...