by Hamdan Zefa | Mar 5, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza lachiwiri (2/1) “Mitala imayambitsa ufiti” Akazi ena amaopa kuvomera kukhala mkazi wachiwiri, wachitatu kapena wachinayi chifukwa choti adamva zoti mkazi woyamba amachita matsenga kapena ufiti kuti awapatse mavuto akazi amene mwamuna wake...
by Hamdan Zefa | Mar 4, 2022 | Featured, Fiqh, Marriage, Misconceptions, Sunnah
Bodza loyamba: “Akazi pa mitala amakhala m’nyumba imodzi” Anthu ena amaganiza kuti mitala ikutanthawuza kuti mwamuna atenge akazi awiri ndikumakhala nawo m’nyumba imodzi, komanso kuti mikangano imene ingakhalepo pakati pa akaziwa itha...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fasting, Fatawa, Featured, Fiqh
KUBWEZA (QADHAA) MASIKU OSIYIDWA PAKUSALA MWEZI WA RAMADHAN Qadhaa ya Swawm ndi chani? Qadhaa ya swawm ndiko kusala kwa munthu yemwe sanasale masiku ena a mwezi wa Ramadhan, kapena kumusalira m’bale wake pambuyo poti munthu wamwalira atasiya swawm yomwe analonjeza kwa...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Fiqh, Salaat
Kuchotsedwa Kwa Kuwerenga Pambuyo Pa Imaam Mu Swalaat/Rakaat Zokweza Mawu Swifatu Swalaat Nabiy salla Allah alaih wasallam (Sheikh Al Albaani) pge 98 Kodi Kuwerenga Surah Al Fatiha kunalolezedwa nthawi yanji nanga kunaletsedwa nthawi yanji? Mtumiki salla Allah alaih...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fasting, Featured, Fiqh, Islam, Sunnah
Kuchokera m’mawu omwe anthu amati ndi ochokera kwa Mtumiki salla Allah alaih wasallam, عن أبي هريرة قال: قال رسول الله ﷺ : أول شهر رمضان رحمة، وأوسطه مغفرة، وآخره عتق من النار. منكر، روه الديلمي Nkhani inachokera kwa Abi Hurairah radhia Allah anhu, anati:...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fatawa, Featured, Fiqh, Islam, Islamic Manners, Marriage, Misconceptions
خـــاتَمُ الخِـــطْبَةِ ENGAGEMENT (WEDDING) RING(Sheikh Naasiru Ddeen Al-Albaani) Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa uyo yemwe Allah anamutumiza kuti adzakwaniritse makhalidwe abwino. Pali zichitochito zina...
Your Comments