Uzair

Uzair anali munthu woyera komanso wanzeru. Anakhala pambuyo pa Mneneri Sulaiman alaih salaam komanso asanabwere Mneneri Zakaria alaih salaam. Tsiku lina monga mwachizolowezi chake, Mneneri anakayendera munda wake pa bulu. Chakumasana, anafika pa kamzinda kena...

Shuaib bun Mikeel

Ma ulamaa akuluakulu amakhulupilira kuti Shuaib alaih salaam anali munthu wachikulire yemwe anateteza Musa alaih salaam. Mneneri Musa alaih salaam anakwatira mwana wa Mneneri Shuaib alaih salaam asanapite ku Egypt. Koma palibe maumboni ovomereza kapena kutsutsa...

Yusha’ bun Nun & Hizqeel bun Budhi

Yusha alaih salaam anali chidzukulu chachikulu cha Mneneri Musa alaih salaam. Anali ndi agogo akewo pa ulendo waukulu wochokera mu Egypt. Musa alaih salaam anali kumkonda mzukulu wakeyu kotero anampatsa ntchito zofunikira zambiri. Anayenda mu chipululu kwa zaka...

Nuh bun Lamak

Allah Subhaanah wa Ta’la anatumiza Mneneri Nuh alaih salaam patadutsa zaka 100 pambuyo pa Mneneri Adam alaih salaam. Chiwelengero cha anthu padziko chinachuluka zedi.Panthawiyi, shaytwaan anawasokoneza anthu kotero anali kupembedza mafano, kotero Allah anatumiza...

Hud bun Shalakh

Pambuyo pa chigumula, anthu a Nuh alaih salaam anachulukana padziko. Mneneri Nuh alaih salaam anali ndi ana komanso zidzulu zambiri, choncho chiwelengero cha anthu padziko chinakula. Ambiri mwa iwo anakhanzikika ku Yemen. Zimakambidwa kuti omwe anakhanzikika kumeneko...

Adam

Kalelake kwambiri, Allah Subhannahu wa Ta’la analenga dzuwa, mwezi ndi nthaka. Pambuyo pake anaona kuti zolenga zake sizikukwanira.Choncho anawatuma Angelo ake kuti atenge dothi pa dziko. Angelo aja anamvera ndipo anapititsa dothi kwa Allah lomwe analengera...