Zopeka – Kuwerenga Qur’an ku Manda

Pali ma hadith omwe anapekedwa nalembedwa mu buku kuti tidziwerenga poikira umboni kuti kuwerenga Qur’an ku Manda ndi Sunnah. Ma hadith amenewa ndi osafunika kuti tidziwagwiritsa ntchito tikawaona. Chifukwa ndi ma hadith oipa omwe amanamizira Mtumiki salla Allah...

Kuvala Nsapato pa Swalat (2)

GAWO LACHIWIRI   Imodzi mwa nkhani zovuta kudzimvesetsa chifukwa cha kuchepekedwa kwa maphunziroku ndi yomwe ndikufuna kulongosola lero…ndipo pankhaniyi ndakhala ndikuona ma sheikh omwe akhala akuyesetsa kuwalongosolera anthu, akunyozedwa poyankhuliridwa...

Kuvala Nsapato pa Swalat (1)

بسم الله الرحمن الرحيم الحمد لله رب العالمين والصلاة والسلام على رسوله الكريم وعلى آله وأصحابه ومن تبعهم إلى يوم الدين أما بعد Pali mitu yomwe imakambidwa ndi ma Sheikh, yomwe ndiyofunikira kwambiriimene munthu amati akangoyankhula, anthu omwe sazindikira –...

Swalat ya Maliro (Janaazah)

Tiyeni titsegule page103 ya chitabu cha أحكام الجنائز وبدعها cha Allaamatu Sheikh Muhammad Naasirul-Deen Al Albaaniy, ndipo tiyambire pa mutu wa number 13 kumapita kutsogolo mmapage otsatira mu chitabuchi Zoyenera kuchita pa Janaaza Janaaza ndi mwambo wa maliro womwe...

Fodya Mchisilamu

Fodya ndi chimodzi mwa zinthu zomwe zangobwera posachedwapa ndipo mbuyomu kunalibe. Nthawi ya Mtumiki salla Allah alaih wasallam kunalibe kugwiritsa ntchito fodya, komanso mbuyo mwakemo nthawi ya Atumiki onse kunalibe. Nthawi ya ma Shawabanso kunalibe fodya,...

Mathero

Pambuyo pa kuwerenga zolembedwa zoyambilira zokhunza amayi, anthu omwe sali Asilamu akhonza kukhala ndi funso lofanana loti: Kodi akazi a Chisilamu lero lino akutengedwa malinga momwe zalembedwera mu bukumu? Yankho lake ndiloti: Ayi. Kopa popeza funso ili sililephera...