Mitala M’chisilamu

Mitala mu Chisilamu si LAMULO LOKAKAMIZIDWA, koma ndi chilolezo kwa yemwe wafuna. Allah Ta’la analoleza mitala mu Surat Al Nisaai Aayah #3. Nkhani ya mitala imavuta mbali zonse; kwa mwamuna ndi kwa mkazi komwe, chifukwa cha kusatsatira ndondomeko komanso...

Kufunsidwa za Deen

Basharul Haafi rahimahu Allah anati: “Yemwe amakonda kuti azifunsidwa (za deen), sali oyenera kufunsidwa” قال بشر الحافي رحمه الله تعالى: مَن أحبَّ أن يُسْأَلَ، فَليسَ بِأَهْلٍ لِأَنْ يُسْألَ. Mau awa ndi akuya zedi. Allah atipatse kumvesetsa Phunziro:...

Good Friday and Easter Monday

The Position of Islam and Muslims on GOOD FRIDAY AND EASTER (Holidays 2nd & 5th April, 2021) For those who love Isa (Jesus) son of Mary ‘Alaihima Ssalaam GOOD FRIDAY is a Christian holiday commemorating the ostensible crucifixion of Jesus and his death at...

Kumasulira Khutbah

KODI NDIZOLOLEDWA KUMASULIRA KHUTBAH YA JUM’AH MUCHIYANKHULO CHINA ZITAKHALA KUTI ANTHU OMVETSERA SAKUVA CHIARABU? Nkhaniyi anthu amasiyana zokamba zenizeni chifukwa choti nthawi ya Mtumiki kunalibe kumasulira, komanso panalibe chifukwa chomasulira khutbah poti...

Dua Yamphamvu

Kuchokera kwa Ibn Abbas radhia Allah anhu: Mtumiki wa Allah (ﷺ) amatuluka mnyumba mwa mkazi wake, Juwayriyyah – dzina lake koyamba linali Barrah, koma anasintha – pamene Mtumiki anatuluka, Juwayriyyah anali pamalo opemphelera mpaka pamene anabwelera....