Phindu la Pemphero la Usiku

Allah Ta’la amayandikira (ndi ulemelero wake) usiku uliwonse pa thambo la dziko lapansi, ndipo amaitana: “kodi alipo yemwe akundipempha ndimuyankhe? nanga alipo yemwe akupempha chikhululuko ndimukhululukire? kodi alipo yemwe akufuna kulapa machimo ake...

I’tikaaf (M’bindikiro)

Pachiyankhulo chabe, mawuwa amatanthauza kubindikira, pamene pa Shariah mawuwa amatanthauza kubindikira munzikiti ndikachitidwe kake, komanso ndichitsimikizo chake, ndicholinga chofuna kudziyandikitsa kwa Allah. Lamulo la I’tikaaf Lamulo la I’tikaaf ndi...

Kuchukucha Mkamwa Utasala

Anzathu ena ambiri akamapanga wudhu sachukucha mkamwa akuti kuwopa kuwononga swaum yawo. Zimenezitu ndizolakwika pazifukwa zambiri: 1. Kuchukucha mkamwa sikuwononga swaum ngati ukupanga wudhu, ngakhale madzi atalowa kukhosi mwangozi swaum yako sinawonongeke. 2. Palibe...

Swalaatul Ghaaib

Imeneyi ndi swalaat yomwe imapempheredwa dera lina lotalikira komwe swalat Janaza yachitikira. Maswalidwe a swalaatul ghaaib ndichimodzimodzi swalaatul janaaza. Komatu swalat imeneyi (swalaatul ghaaib) ili ndi malamulo osiyana ndi swalaatul janaza makamaka pa munthu...

Kuvala Nsapato pa Swalat (2)

GAWO LACHIWIRI   Imodzi mwa nkhani zovuta kudzimvesetsa chifukwa cha kuchepekedwa kwa maphunziroku ndi yomwe ndikufuna kulongosola lero…ndipo pankhaniyi ndakhala ndikuona ma sheikh omwe akhala akuyesetsa kuwalongosolera anthu, akunyozedwa poyankhuliridwa...

Kuvala Nsapato pa Swalat (1)

بسم الله الرحمن الرحيم الحمد لله رب العالمين والصلاة والسلام على رسوله الكريم وعلى آله وأصحابه ومن تبعهم إلى يوم الدين أما بعد Pali mitu yomwe imakambidwa ndi ma Sheikh, yomwe ndiyofunikira kwambiriimene munthu amati akangoyankhula, anthu omwe sazindikira –...