by Admin | Dec 10, 2020 | Fatawa, Featured, Fiqh, Salaat
KODI NDIZOLOLEDWA KUMASULIRA KHUTBAH YA JUM’AH MUCHIYANKHULO CHINA ZITAKHALA KUTI ANTHU OMVETSERA SAKUVA CHIARABU? Nkhaniyi anthu amasiyana zokamba zenizeni chifukwa choti nthawi ya Mtumiki kunalibe kumasulira, komanso panalibe chifukwa chomasulira khutbah poti...
by Admin | Aug 5, 2020 | Fatawa, Featured
Kudya dothi ndi chizolowezi chosafunikira chomwe chimachitika ndi azimai ngakhalenso ana ena. Nthawi zina chimakhala chikhalidwe chotengera, pomwe nthawi zina zikhonza kubwera kuchokera mu condition inayake yamthupi, monga kusowa kwa michere ina makamaka iron....
by Admin | Jul 26, 2020 | Fatawa, Featured, Islam
Mafunso omwe timafunsa pa za deen timafuna kudziwa kuti kodi deen yathu tiyendetse bwanji. Timafuna kudziwa kuti kodi ibaada tingachite bwanji, nanga chikhulupiliro chathu tingachisamale bwanji. Kudzera mu kufuna kudziwa zinthu momwemo, ambiri tili ndi chizolowezi...
by Admin | Jul 18, 2020 | Fatawa, Islam
Kodi Chisilamu chikutinji kumbali ya kuwonera ma filimu a deen? Mchisilamu mulibe ma filimu, pazifukwa izi: 1. Chifukwa kupanga ma film kunachokera kwa ma kuffaar omwe njira yomwe amapangira makafirimu awo, ndiyoyenera malinga ndi iwowo; palibe njira yoyenera malinga...
by Admin | Jan 13, 2020 | Fatawa
بسم الله الرحمن الرحيم ٱلْيَوْمَ أُحِلَّ لَكُمُ ٱلطَّيِّبَٰتُۖ وَطَعَامُ ٱلَّذِينَ أُوتُوا۟ ٱلْكِتَٰبَ حِلٌّ لَّكُمْ وَطَعَامُكُمْ حِلٌّ لَّهُمْۖ وَٱلْمُحْصَنَٰتُ مِنَ ٱلْمُؤْمِنَٰتِ وَٱلْمُحْصَنَٰتُ مِنَ ٱلَّذِينَ أُوتُوا۟ ٱلْكِتَٰبَ مِن قَبْلِكُمْ إِذَآ...
by Admin | Jan 13, 2020 | Fatawa
Funso: Kodi ndichifukwa chani akazi wa Chisilamu tikamawafunsira amanyada kwambiri ndipo akakulola amapanga zamwano zoyelekedwa, ndye tikamakwatira achikunja ndikulakwa ?? Yankho: Allah Ta’la akunena mu Qur’an kuti: وَمَا كَانَ لِمُؤْمِنٍ وَلَا مُؤْمِنَةٍ...
Your Comments