by Admin | Sep 3, 2021 | Fiqh, Islam, Misconceptions, Salaat
Anthu ambiri akamaliza swalah za faradh ndikumaliza kupanga ma Adhikaar, amanyamula manja awo ndikuyamba kupanga Dua pagulu kapena payekhapayekha aliyense. Ndipo pali gulu la anthu ena omwe samapanga, koma amati akamaliza kupanga ma adhkaar basi amatuluka, poti ma dua...
by Admin | Sep 3, 2021 | Featured, Fiqh, Misconceptions
Kuyamikidwa konse nkwa Allah, Yemwe ananena kuti: Watukuka ndi kudalitsika (Allah) Amene m’manja Mwake muli ufumu (wochita chilichonse pazolengedwa zonse); ndipo Iye ali ndi mphamvu yokwanira pachilichonse. Amene adalenga imfa ndi moyo kuti akuyeseni (mayeso) ndani...
by Admin | Sep 3, 2021 | Featured, Misconceptions
KUCHOTSA CHIKAIKO PA KUSOKONEKERA KWA ANTHU ENA PA MATANTHAUZO A ENA MWA MA AAYAH A MU QUR’AN YOLEMEKEZEKASurah Ad Dhuha (Aayah #7) وَوَجَدَكَ ضَالًّا فَهَدَى – الضحى 7 “Ndipo adakupeza uli wosazindikira (Qur’an) nakuongola (pokuzindikiritsa Qur’aniyo ndi malamulo a...
by Admin | Sep 3, 2021 | Uncategorized
Hijaama ndi liwu la Chiarabu lomwe likutanthauza muchiyankhulocho kuti “kuyamwa”, monga mmene timayankhulira kuti “mwana akuyamwa bere la mai ake” حجم الطفل ثدي أمه أو مص الطفل ثدي أمه Tsopano liwu loti حجم Likutanthauza size, ndipo likugwiritsidwa ntchito chifukwa...
by Admin | Apr 8, 2021 | Fasting, Featured, Fiqh
Kuyambikidwa konse nkwa Allah Mwini zolengedwa zonse, Mtendere ndi Madalitso zipite kwa Mtumiki wake wolemekezeka. Kodi tikhonzekere motani mwezi wa Ramadhan? Pamene tili pa chitseko cha mwezi wa Ramadhan, aliyense mwa ife akuyenera kuti akudziwa komwe akupita...
Your Comments