“Hijaamah” Ndichiyani?

Hijaama ndi liwu la Chiarabu lomwe likutanthauza muchiyankhulocho kuti “kuyamwa”, monga mmene timayankhulira kuti “mwana akuyamwa bere la mai ake” حجم الطفل ثدي أمه أو مص الطفل ثدي أمه Tsopano liwu loti حجم Likutanthauza size, ndipo likugwiritsidwa ntchito chifukwa...

Kuloleza Zoletsedwa -Nyimbo

Kuzikongoletsa zinthu za haram nkuzisandutsa kukhala za halaal popanda umboni kuchokera mu Qur’an ndi Sunnah: KUIMBA NDI KUMVERA NYIMBO Abu Turaab Adhwaahiri analemba article mu magazine yotchedwa Al-Raaid kuti: Qur’an ndi Sunnah sizinaletse nyimbo,...