by Admin | Sep 5, 2021 | Featured, Shia
HUSAIN .. MADAD YA HUSAIN .. YA HUSAIN !! Nchifukwa chani ma Shia amatamanda ndi kulemekeza Husain (رضي الله عنه) yekha ndi kusiya ana ena onse a Ali (رضي الله عنه)? Kodi munayamba mwadzifunsapo funso limeneli? Nanga nkhani imeneyi inayamba yakudabwitsanipo?...
by Admin | Sep 4, 2021 | Fasting, Fatawa, Featured, Fiqh
KUBWEZA (QADHAA) MASIKU OSIYIDWA PAKUSALA MWEZI WA RAMADHAN Qadhaa ya Swawm ndi chani? Qadhaa ya swawm ndiko kusala kwa munthu yemwe sanasale masiku ena a mwezi wa Ramadhan, kapena kumusalira m’bale wake pambuyo poti munthu wamwalira atasiya swawm yomwe analonjeza kwa...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Shia
KODI MA SHIATU RAAFIDA NDI ASILAMU OKHULUPILIRA?Pomwe iwo anapanga shahaada ndipo amaikira umboni kuti palibe wopembedzedwa mwachoonadi kupatula Allah, ndikuti Muhammad ndi Mtumiki wake, komanso Qibla yawo ndi ku Makkah ndipo amaswali munsikiti? Siyense yemwe wapanga...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Fiqh, Salaat
Kuchotsedwa Kwa Kuwerenga Pambuyo Pa Imaam Mu Swalaat/Rakaat Zokweza Mawu Swifatu Swalaat Nabiy salla Allah alaih wasallam (Sheikh Al Albaani) pge 98 Kodi Kuwerenga Surah Al Fatiha kunalolezedwa nthawi yanji nanga kunaletsedwa nthawi yanji? Mtumiki salla Allah alaih...
by Admin | Sep 4, 2021 | Featured, Islam, Misconceptions
Kuchokera mu Minhaajul Qaaswideen fi Fadhlil Khulafaai Rraashideen page 187, tidziwa kuti nawo ma Khawaarij amadana ndi ena mwa ma Swahaba. Khawaarij ndigulu la anthu omwe anali limodzi ndi Ali radhia Allah anhu pa nkhondo zake, koma anamutuluka ndikumuwukira pamene...
Your Comments