Mafunsidwe a Mahr

Zomwe zimachitika masiku ano zobisa mahr nkudzaitanitsa nthawi yomwe nikaah ikuchitika, si chiphunzitso cha Chisilamu, komanso mboni ziwiri kufunsa mahr tsiku la nikaah sichiphunzitso cha Chisilamu. Mahr imayenera kukhala ikudziwika kwa waliyy (muyang’aniri wa mkazi)...

Ndondomeko ya Nikaah

Zofunika pa nthawi ya nikaah Pangani Download PDF yake Okwatira Pamene mwambo wa nikaah ukuchitikira malo aliwonse omwe anthu asankha (monga munsikiti, m’nyumba ngakhalenso mu office ya Sheikh), malo aliwonsewo omwe tikufuna kuchitiramo mwambo wa nikaah siziri...

Kodi Mtsikana Angavale Niqaab?

Mtsikana wa Chisilamu akatha msinkhu ndiokakamizidwa kuvala Hijaab ngakhale niqaab monga mmene ali okakamizidwira kugwira ntchito zina zonse cha Chisilamu monga swalaat swiyaam ndi zina zotero. Tikamati Hijaab, sitikutanthauza kampango kamene mumavala kumutuko ayi,...

Kutanthauzira Maloto

Maloto amachitika pamene munthu wagona tulo ndipo mzimu wake umachoka mthupi ndikupita kwina  kumene atha kukakumana ndi mizimu ya anthu ena, omwalira kapena amoyo omwe ali mtulo ngati iyeyo. Choncho Allah amangosiya connection pakati pa thupi ndi mzimu wake, ndipo...

What is Salafi

All praise is due to Allah alone, and peace and blessings be upon the Messenger, his family and his Companions.To proceed: “As-Salafiyyah” is an attachment or affiliation to the ‘Salaf’. And “The Salaf” are the Companions of the...