Kodi Ziwanda (Majinn) Zimafa?

Tikudziwa bwinolomwe kuti ena mwa majinn ndi ma shaytwaan (asatana), amenewa ndi ma jinn oipa, ndipo asatanawa amafa mmene amafera majinn ndi anthu. Onsewa akulowa mukuyankhula kwa Allah Ta’ala koti:  كُلُّ مَنْ عَلَيْهَا فَانٍ – وَيَبْقَى وَجْهُ رَبِّكَ...

Kuchulukitsa Kulumbira Poyankhula

Pali anthu ena anazolowera kulumbira m’Dzina la Allah, mwachitsanzo kunena kuti “Wallahi…”, ndipo amachitenga kukhala chizolowezi chawo pakuyankhula kulikonse, zofunikira ngakhale zosafunikira. Chizolowezi choterechi ndicholakwika kwambiri....
Mliri Sudzalowa m’Madinah

Mliri Sudzalowa m’Madinah

KUCHOTSA KUSAMVETSETSA PA MA HADITH OMWE ABWERA KUTI “MLIRI SUDZALOWA MU MZINDA WA MADINAH” (Abu Shareef C Idris) Download PDF>> الحمد لله، القائل ﴿ أَحَسِبَ النَّاسُ أَنْ يُتْرَكُوا أَنْ يَقُولُوا آمَنَّا وَهُمْ لَا يُفْتَنُونَ ﴾ وقال ﴿...

Swalaatul Ghaaib

Imeneyi ndi swalaat yomwe imapempheredwa dera lina lotalikira komwe swalat Janaza yachitikira. Maswalidwe a swalaatul ghaaib ndichimodzimodzi swalaatul janaaza. Komatu swalat imeneyi (swalaatul ghaaib) ili ndi malamulo osiyana ndi swalaatul janaza makamaka pa munthu...

Yemwe Amachotsa Ziwanda

Funso: Kodi nchifukwa chani anthu amakonda kufunsa kuti “ndikufunafuna Sheikh omwe amachotsa ziwanda, amene ali ndi number yawo anditumizire?” Yankho: Amafuna kuti akawawelengere Qur’an, ma Dua ndi ma Dhikr chifukwa iwowo sadziwa, komanso safuna...

Kutanthauzira Maloto

Maloto amachitika pamene munthu wagona tulo ndipo mzimu wake umachoka mthupi ndikupita kwina  kumene atha kukakumana ndi mizimu ya anthu ena, omwalira kapena amoyo omwe ali mtulo ngati iyeyo. Choncho Allah amangosiya connection pakati pa thupi ndi mzimu wake, ndipo...