Kupereka Fatwa Pazinthu Zosachitika

Mafunso omwe timafunsa pa za deen timafuna kudziwa kuti kodi deen yathu tiyendetse bwanji. Timafuna kudziwa kuti kodi ibaada tingachite bwanji, nanga chikhulupiliro chathu tingachisamale bwanji. Kudzera mu kufuna kudziwa zinthu momwemo, ambiri tili ndi chizolowezi...

Muli Gulu Lanji M’Chisilamu?

Ndimafunsidwa kawirikawiri: “…ndinu wa Sunni … Qadriyya … Shia … Ashaaira … kapena Muutazila?? Koma ine mainawa ndimangomva sindikudziwa kuti ndichani. Ndiye ndimafuna ntadziwa kuti zikutanthauza chani, komanso ndikufunikira kwanji...

Wahabiyah Ndichani?

Msilamu asamalimbane ndi kutsatira maina, magulu kapena zirizonse zomwe zikuonetsa kugawika kwa Ummah. Koma ndizofunika kwa iye kuzidziwa munjira ya kuphunzira, akadziphunzira afalitse choona chenicheni chomwe Asilamu atsatire. Imeneyo ndiye Da’wah ya Sheikh...

Zopeka za Pamaliro (Bid’ah)

1. Imaam kupanga dua ya pagulu pambuyo pa swalat Janaazah.  Palibe chiphunzitso choti imaam akaswalitsa swalat Janaazah apange dua anthu nkumavomera kuti Ameen.  2. Kuimba kapena kupanga ma adhkaar mokweza poperekeza kumanda Imeneyi si sunnah ya Mtumiki ndi...

Zithunzi

Nkhani ya zithunzi ndi yaitali chifukwa imakhudza mbali zambiri zomwe zimakhala zosiyana zigamulo zake,  monga kukhala zoletsedwa kapena zololedwa kapena kuletsedwa kotheratu, mopanda kupatula komanso kuletsedwa kopatula. Pali ma aayah a mu Qur’an komanso...

Mafilimu a Chisilamu

Kodi Chisilamu chikutinji kumbali ya kuwonera ma filimu a deen? Mchisilamu mulibe ma filimu, pazifukwa izi: 1. Chifukwa kupanga ma film kunachokera kwa ma kuffaar omwe njira yomwe amapangira makafirimu awo, ndiyoyenera malinga ndi iwowo; palibe njira yoyenera malinga...