by Admin | Jan 22, 2019 | Fiqh, Zakaat
Kuyamikidwa ndi kwa Allah ndipo mtendere ndi madalitso zikhale pa Mtumiki wathu Muhammad salla Allah alaih wasallam,,,amma ba’d Mukuona kwanga ndapeza kuti chiwelengero cha Asilamu ambiri sakumapereka Zakaat kuno ku Malawi. Ndipo izi sichifukwa choti anthuwo...
by Admin | Jan 21, 2019 | Featured, Salaat
Ambiri masiku ano amasokonezeka nthawi ya swalat yomwe anaphunzitsa Mtumiki salla Alaih waallam, ndi wotchi makamaka akapita dziko lina. Ena anati “mzikiti womwe timaswali kuno ndi wa Mashia chifukwa akumachita adhaan ya Dhuhr past 1, pomwe ku Malawi...
by Admin | Dec 24, 2018 | Fiqh
بسم الله الرحمن الرحيم Kugawa Chuma Chosiyidwa Malinga ndi Qur’an Yolemekezeka Munthu akamwalira nkusiya chuma, Asilamu akuyemera kugawa chumacho moyenera ndi abale ake omwe wasiya omwalirayo. Nzomvetsa chisoni masiku ano munthu ali ndi makolo ake, azibale ake,...
by Admin | Dec 21, 2018 | Fiqh
Zinthu Zofunikira Kuti Yemwe Akufuna Kuphunzira Ayambilire Kuchita Kuti Adziteteze Phunziro limeneli likuchokera pa mutu woti “Ahlu Ssunnati wa ‘alaamaatihim” Sheikh Rabieu bun Haadi Al Madkhali Kufunafuna maphunziro mu deen ndi lamulo kwa wina...
by Admin | Dec 17, 2018 | Fiqh
Tiwadziwe ma Imaam a Madh’hab Anayi 1. Imaam Abu Hanifa AlNu’man bun Thabit 2. Imaam Maalik bun Anas 3. Imaam Muhammad bun Idris AlShaafi’iy 4. Imaam Ahmad bun Hanbal Anthu amene amatsatira Qur’an ndi Sunnah za Mtumiki salla Allah alaih...
by Admin | Nov 13, 2018 | Fiqh
Ndi chifukwa chani timayenera kutsuka ndi mchenga kamodzi? “Kuyeretsa kwa chiwiya chanu chomwe wanyambitamo galu ndi kutsuka ka 7, kamodzi kakeko ndi mchenga”. Tonse tikudziwa kuti Mtumiki anatiuza kuti tidzitsuka chiwiya chomwe galu wanyambita ka seven,...
Your Comments