by Admin | May 7, 2020 | Salaat, Sunnah
Allah Ta’la amayandikira (ndi ulemelero wake) usiku uliwonse pa thambo la dziko lapansi, ndipo amaitana: “kodi alipo yemwe akundipempha ndimuyankhe? nanga alipo yemwe akupempha chikhululuko ndimukhululukire? kodi alipo yemwe akufuna kulapa machimo ake...
by Admin | May 7, 2020 | Fasting
Pachiyankhulo chabe, mawuwa amatanthauza kubindikira, pamene pa Shariah mawuwa amatanthauza kubindikira munzikiti ndikachitidwe kake, komanso ndichitsimikizo chake, ndicholinga chofuna kudziyandikitsa kwa Allah. Lamulo la I’tikaaf Lamulo la I’tikaaf ndi...
by Admin | May 6, 2020 | Fasting, Featured, Fiqh
Anzathu ena ambiri akamapanga wudhu sachukucha mkamwa akuti kuwopa kuwononga swaum yawo. Zimenezitu ndizolakwika pazifukwa zambiri: 1. Kuchukucha mkamwa sikuwononga swaum ngati ukupanga wudhu, ngakhale madzi atalowa kukhosi mwangozi swaum yako sinawonongeke. 2. Palibe...
by Admin | Feb 17, 2020 | Featured, Fiqh, Islam
Imeneyi ndi swalaat yomwe imapempheredwa dera lina lotalikira komwe swalat Janaza yachitikira. Maswalidwe a swalaatul ghaaib ndichimodzimodzi swalaatul janaaza. Komatu swalat imeneyi (swalaatul ghaaib) ili ndi malamulo osiyana ndi swalaatul janaza makamaka pa munthu...
by Admin | Feb 16, 2020 | Featured, Islam
Funso: Kodi nchifukwa chani anthu amakonda kufunsa kuti “ndikufunafuna Sheikh omwe amachotsa ziwanda, amene ali ndi number yawo anditumizire?” Yankho: Amafuna kuti akawawelengere Qur’an, ma Dua ndi ma Dhikr chifukwa iwowo sadziwa, komanso safuna...
Your Comments