by Admin | Jun 15, 2019 | Fiqh, Islam
Malangizo a Mtumiki salla Allah alaih wasallam kwa Atsogoleri a magulu a nkhondo: كانَ رَسولُ اللهِ صَلَّى اللَّهُ عليه وَسَلَّمَ إذَا أَمَّرَ أَمِيرًا علَى جَيْشٍ، أَوْ سَرِيَّةٍ، أَوْصَاهُ في خَاصَّتِهِ بتَقْوَى اللهِ، وَمَن معهُ مِنَ المُسْلِمِينَ خَيْرًا، ثُمَّ...
by Admin | Jun 14, 2019 | Fiqh, Islam
Funso: “Kodi nchifukwa chani mu ulaliki wa ma Khawaarij munasankha kupereka chitsanzo nkhani ya Usama? mesa anali Msilamu? simukuona kuti anthu adziwona ngati mukumufukula zinsinsi zake kapenanso kumuweruza komans kuipitsa mbiiri yake? Komanso ambiri...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Kusiyana kwa Manhaj ndi Aqeedah Timamva ma Sheikh akamalalikira akunena kuti “Mahnaj Ahli Sunnah wal Jamaa”, ndipo nthawi zina timamva akunena kuti “Aqeedatu Ahli Sunnah wal Jamaa”. Kodi mau awiriwa “Manhaj ndi Aqeedah” ndi...
by Admin | May 6, 2019 | Islam
Nthawi zambiri timakhala tikulimbikira kuchenjeza za bid’ah chifukwa ndi chinthu choopsa mu deen kuposa kuchita tchimo. Msilamu aliyense akuyenera kuidziwa bid’ah mokwanira kuti aipewe. Komanso monga momwe tikudziwira, cholinga chathu chachikulu ndi...
by Admin | May 2, 2019 | Islam
Kusintha dzina la bambo ndikutenga la mwamuna wake pambuyo pa kukwatiwa Mkazi kusintha dzina labambo ake ndikutenga la munthu wina wake ndi kulakwa kwakulu. Dzina la bambo limalongosola chibale cha kobadwira (lineage),, tsopano mkazi akasintha dzina la bambo ake...
by Admin | Jan 25, 2019 | Islam
Kukhulupirika Pa Maphunziro a Chisilamu الإخلاص في طلب العلم Taonani kukhulupirika komwe kunali ndi ma Imaam amene Allah Subhaanah wa Ta’ala anawalandira ntchito zawo pa dziko la pansi ndi kumwamba: Ndingokupatsani chitsanzo cha Imaam mmodzi, Imaam Al...
Your Comments