by Admin | Nov 11, 2019 | Featured, Salaat
Tiyeni titsegule page103 ya chitabu cha أحكام الجنائز وبدعها cha Allaamatu Sheikh Muhammad Naasirul-Deen Al Albaaniy, ndipo tiyambire pa mutu wa number 13 kumapita kutsogolo mmapage otsatira mu chitabuchi Zoyenera kuchita pa Janaaza Janaaza ndi mwambo wa maliro womwe...
by Admin | Jul 23, 2019 | Hajj
Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Munayamba mwaziwona nkhunda mazanamazana zitatera paphiri ndi mawonekedwe ake odziwika ndi aliyense, omwe amasonyeza mtendere, chikondi komanso mgwirizano? Kumakkah, paphiri la Arafah mukhoza kukhala osangalatsidwa komanso...
by Admin | Jul 23, 2019 | Hajj
Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Twawaaf (Tawaf) ndi liwu la chinenero cha chiarab lomwe limatanthauza kuzungulira, ndipo malingana ndi malamulo a Hajj mchisilamu, liwuli limatanthauza kuzungulira nyumba yolemekezeka ya Ka’bah. Tawaf ili...
by Admin | Jul 23, 2019 | Hajj
Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Munthu ofuna kupanga hajj ayenera kutsimikiza imodzi mwa mitundu ya Hajj iri m’munsiyi asanalowe mu Ihram pofuna kupanga Hajj. Mitundu yake ndi iyi: Ifrad (Yapayokha) yomwe imatanthauza kupanga Hajj yokha. Qiran...
by Admin | Jul 23, 2019 | Hajj
Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Qur’an yolemekezeka ikutifotokozera kuti Mneneri Ibrahim adalamulidwa ndi Allah kuti alengeze ndi kuwawuza anthu za Hajj, omwe mu lamulo la Mulungu adzavomera kuyitana kwa Mwini lamulo ndipo adzakonza maulendo...
by Admin | Jul 23, 2019 | Hajj
Hajj ndi Chiyani? Dowload PDF (direct link) Listen/Download MP3 Poyambilira ndikumuyamika Allah Subhaanah wa Ta’ala Mbuye wa zolengedwa zonse. Yemwe anayipanga Hajj kukhala imodzi mwa nsichi zomwe zamanga chipembedzo cha chisilamu yomwe mkati mwake Asilamu...
Your Comments