Ufulu wa Kusankha

Anthu anaika freedom of choice pa kukwatira ndikukhala pa banja lovomerezeka, chifukwa chopangidwa influence ndi ma ideologies a ku west omwe adadza kudzalimbana ndi malamulo a Deen ya Chislamu, omwe amatsutsa kalikonse ponena kuti Chisilamu chimapondereza ufulu wa...

Sindidzakwatira/wa Mpaka Kale

Gawo Loyamba: Banja ndi chinthu chofunika kuchikhonzekera pambuyo pa imfa pamoyo wadziko lapansi, chifukwa banja: 1. Limakulowetsa mu chikhalidwe chatsopano chomwe umalidzire nacho moyo wapadziko. 2. Komanso banja ndi chinthu chomwe chimamukwaniritsira munthu half ina...

Kuwerenga Zitabu za Bid’ah

Kodi zoona ndi ziti pa nkhani ya kuwerenga zitabu za bid’ah komanso kumvera ma audio a ma Sheikh a bid’ah? Sizololedwa kwa munthu oyamba kumene kuphunzira, kapena yemwe sakuzindikira mokwanira; kuwerenga zitabu za bid’ah (zitabu zomwe zikukamba...

Oyenera Kupanga Da’wah

Anthu ena amaganiza kuti Da’wah (kuitanira kwa Allah) palibe yemwe angapange kupatula ma ulamaa okhaokha, ndipo omwe akuphunzira kwa ma Ulamaawo sakukakamizidwa kupanga Da’wah. Mutithandiza bwanji pa zimenezi?    Sikuti ndi maganizo chabe, koma ndizoona....
Bwalo la Fataawa

Bwalo la Fataawa

Kutulutsa zinthu za mu Mzikiti Sizololedwa kutulutsa zinthu za mu mzikiti kukadzigwiritsira ntchito malo ena osakhala munzikiti momwemo. Kubwereka mkeka, kapena Qur’an kaya mabuku aliwonse komanso china chirichonse chomwe chinaikidwa mu mzikiti kuti...
Zoletsedwa mu Nasheed

Zoletsedwa mu Nasheed

Kodi kuimba ma Nasheed ndikololedwa? Allah atipatse kuzindikira ********************** Ma nasheed omwe akuimbidwa mzaka zathu zino, ambiri ndi oletsedwa chifukwa akupezeka kunja kwa malamulo (ma condition) a nyimbo zololedwa omwe anabwera kale.   Nasheed ndi...