by Admin | Jan 1, 2019 | Islam
Ambiri mwa ife timakhala tikufunafuna barakah (madalitso) kuchikera mu nambala ya 786 poilemba pamayambiliro pa ma kalata, nkhani, pa grocery komanso malo ambiri. Ena mwaife timailemba nambalayi pa china chane ndikuchikoleka pa galimoto kuti itetezedwe ku ngozi. Ena...
by Admin | Dec 19, 2018 | Islam
“ndipo akakufunsa akapolo anga za ine, ndithu ine ndili pafupi ndimayankha Dua ya opanga dua (kuitana kwa oitana)” Chisilamu chinalongosola ma condition/zofunika kuti kuti Dua iyankhidwe, komanso chinafotokoza zomwe zimaletsa kuti Dua iyankhidwe. Komanso...
by Admin | Dec 2, 2018 | Islam
الفتاوى الشرعية في القضايا العصرية #ص٨٢-٨٥ Fatawa Al Shar’iyya fil Qadhaayal ‘Asriya Page 82-85 “Kumuchita munthu kaafir yemwe ali osayenera kumuchita kaafir sizololedwa. Amene akuyenera kumuchita kaafir ndi amene ali oyenera kumuchita kaafir. Amene...
by Admin | Nov 19, 2018 | Islam
Ngati makolo athu kapena abale athu ali ma kafir, tisawachite kukhala atetezi athu E inu amene mwakhulupirira! Musawachite makolo anu ndi abale anu kukhala atetezi anu ngati (iwo) akukonda kusakhulupirira Mulungu m’malo mokhulupirira (kukhala Asilamu). Ndipo mwa...
by Admin | Nov 11, 2018 | Islam
HUSSEIN .. MADAD YA HUSSEIN .. YA HUSSEIN !! Nchifukwa chani ma Shia amatamanda ndi kulemekeza Hussein (رضي الله عنه) yekha ndi kusiya ana ena onse a Ali (رضي الله عنه)? Kodi munayamba mwazifunsapo funso limeneli? Nanga nkhani imeneyi inayamba yakudabwitsanipo?...
by Admin | Nov 9, 2018 | Islam
Ine ndapanga machimo ambiri ndipo ndikufuna kubwelera kwa Allah ndikupanga tawba, kulapa koona. Kodi ndingapange bwanji tawbah imeneyi Tawbah (Kulapa) ndi kokakamizidwa kwa Msilamu aliyense, ngakhaletu kwa makafiri. Munthu aliyense yem,we wafika msinkhu wolembedwa...
Your Comments