by Admin | Nov 8, 2018 | Islam
Mzimayi ndi okakamizidwa (Faradh) kubisa thupi lonse kupatula nkhope yake ndi manja ake. Ili ndi lamulo la Chisilamu lomwe mzimai wa Chisilamu akuyenera kutsatira ndipo palibe kupatula. Ena amanena kuti hijab ndi choice (kuisanklha kwawo)..ayi ndithu, kuteroko...
by Admin | Nov 8, 2018 | Islam
Kodi Istikhaarah ndi chani? Istikhaarah mu chiyankhulo cha Arabic Kumeneku ndi kupempha kusankha kwabwino pa chinthu. Amanena kuti: “pempha chisankho kwa Allah ﷻ , akusankhira”. Istikhaarah mu Deen Kupempha kusankha, kapena kuti kupempha kuti akuchotsere...
by Admin | Nov 7, 2018 | Islam
Buku la Fazail e Amaal (Fadhwailul A’maal) فضائل الأعمال “Maubwino a Ntchito za Bwino” “Sheikh Muhammad Zakariya Kandhlawi” download source Buku la Fadhaailul A’maal (فضائل الأعمال), lomwe pachiyambi linkatchedwa Tablighi...
by Admin | Nov 7, 2018 | Islam
Jamaatun Tablighi ndi gulu lomwe limagwira ntchito yofalitsa uthenga wa Allah kudzera mu liwu la Tawhid, kalimah Laa ilaaha illa Allah “Tableegh تبليغ Kufalitsa” Ntchitoyi ndi yotamandika ndipo ndi ya malipiro aakulu. Msilamu aliyense ndi udindo wake...
by Admin | Nov 7, 2018 | Islam, Sunnah
Funso Loyamba: Assalaam Alaykum Shekhy! Kodi ndi zizindikiro zanji zomwe amaonetsa mwana wamng’ono pomwe walozedwa ndiye wawelengeredwa ma Aayat a Ruqya; tingadziwe bwanji kuti ufitiwo watha? Funso Lachiwiri: Kodi mwana wamng’ono oti sayankhula ndiye...
by Admin | Oct 30, 2018 | Islam
A Syrian Arabic Calligraphist “Uthman Abduh Hussein Taha Al-Halaby” Leader of all Arabic Calligraphers Born in San’dy Village, Aleppo (Halab) – Syria Full name: Uthman ibn Abduh ibn Husayn ibn Taha Alkurdi. Born in 1934 in a rural area...
Your Comments