Salaat Laylatul Qadr

Swalaat Laylatul Qadr…?? Kuchokera mu Sahih Al Bukhari ndi Muslim, Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam anati: “Yemwe waima kupemphera usiku wa Lailatul Qadr mwa chikhulupiliro (Imaan) komanso moyembekeza malipiro, amakhululukidwa machimo ake”...

Kupemphera Usiku

Allah Ta’la amayandikira (ndi ulemelero wake) usiku uliwonse pa thambo la dziko lapansi, ndipo amaitana: “kodi alipo yemwe akundipempha ndimuyankhe? nanga alipo yemwe akupempha chikhululuko ndimukhululukire? kodi alipo yemwe akufuna kulapa machimo ake...

Zakaat ya Ndalama – Nisaab

Mu gawo lapita lija taona Nisaab ya ndalama komaso ndalama zomwe umafunika kupereka ngati ndalama zokwana pa Nisaab zazungulira chaka. Mmene tinaonela muja, Nisaab imapezeka kuti ndi MK 221,000 potengera nisaab ya siliva. Zomwe zimaonetsa kuti anthu ambiri tili mu...

Zakaat ya Ndalama

Kapelekedwe ka Zakaat ya ndalama. Kodi Nisaab ya ndalama ndi zingati? Chaka chimazungulira bwanji pa Zakaat za ndalama? Ndi ndalama zingati zomwe umapeleka pa ndalama yomwe ulinayo? Tinalongosola mu chigawo chapita kuti Zakaat ya ndalama imachokera pa golide komaso...

Chuma Chopelekera Zakaat

(Olemba: Ibn Muwahhid) Chuma chomwe timapelekera Zakaat tutha kuchigawa patatu. 1. Ndalama 2. Katundu 3. Za ulimi Tiyamba kuona gulu lilironse bwinobwino kuti ndiziti zomwe ziperekedwe mmagawo amenewa 1. Ndalama Ndalama zomwe munthu uli nazo zimayenera kuperekedwa...

Ruqya Mmwezi wa Ramadhan

Timamva kuti shaytwaan amamangidwa mwezi wa Ramadhan, kodi ruqya yochotsa ziwanda ndiyololedwa kupanga mwezi wa Ramadhan? Ngati zili zololedwa, ziwanda zingapezeke bwanji? Ruqya ndiyololedwa kupanga nthawi iriyonse, tsiku lirilonse komanso mwezi uliwonse. Palibe...