Kugwiritsa Maphunziro

Kugwiritsa Maphunziro

Kugwiritsa Maphunziro Pakati Pa Achichepere” Kuchokera mu “Al Kabeer wal Awsat” ya Al Tabarani, anati kuchokera kwa Abi Umaya Al Jumahi radhia Allah anhu: “إن من أشراط الساعة – وفي رواية: ثلاثاً: إحداهن – أن يُلتمس العلم عند...
Kugwiritsa Maphunziro

Kuchoka kwa Maphunziro

Kuchoka kwa ‘ilm komanso kufalikira kwa Umbuli Mtumiki Muhammad salla Allah alaih wasallam analongosola kuti kuchoka kwa maphunziro ndi kuonekera kwa umbuli komanso kufalikira pakati pa anthu ndi chizindikiro cha kutha kwa nthawi. Al Bukhari ndi Muslim (Allah...
Kukhala ndi Munthu Osiya Chisilamu

Kukhala ndi Munthu Osiya Chisilamu

Funso: “Mwamuna achoke muchipembedzo chake cha Chisilamu mkumtsatira muchipembedzo chake (ndikhulupilira mukutanthauza kumtsatira mkazi). Ndafunsa funsoli chifukwa ndakhala ndikuona ambiri kuno ku Joni akupanga zimenezo akuti chifukwa chofuna kukhala mwa...
Mapata Atatu

Mapata Atatu

Mapata Atatu Omwe Munthu Akuyenera Kuwadziwa Buku Lotanthauziridwa Mchichewa, kuchokera mu Buku la  Thalaathatul Usool wa Adillatuhaa, lolembedwa ndi Muhammad bun Abdul Wahab bun Sulaymaan Al Tamimiy Zindikira – akumvere chisoni Allah – kuti tikuyenera...

Calendar ya chi Roma

… New Gallery 2019/1/1CalendarGregorian Calendar الْحَمْدُ لِلَّهِ الَّذِي خَلَقَ السَّمَاوَاتِ وَالْأَرْضَ وَجَعَلَ الظُّلُمَاتِ وَالنُّورَ ۖ ثُمَّ الَّذِينَ كَفَرُوا بِرَبِّهِمْ يَعْدِلُونَ Pamene chaka cha anzathu a chi Roma chomwe timagwiritsa nawo ntchito...
The Innovation of 786

The Innovation of 786

Some of us seek barakah (blessing) from it by writing this number on the top of our letters, documents, exams, and job applications. Some of us write it on something and hang it in the car to ‘protect’ us from accidents. Some of us chose it as the number...