by Admin | May 15, 2019 | Fasting
أعوذ بالله من الشيطان الرجيم بسم الله الرحمن الرحيم الحمد لله رب العالمين رب كل شيئ ومالكه وسع كل شيئ علما، والصلاة والسلام على سيد صاحب الشرف من المرسلين وآله وأصحابه وتابعيه وجميع من اهتدى بهديه إلى يوم الحشر أما بعد يقول الله تعالى وَلاَ تَقْرَبُواْ الزِّنَى...
by Admin | May 2, 2019 | Fiqh
KULERA Uku ndiko kutalikitsa nyengo ya pakati pa ana awiri, komanso kuika malire a chiwelengero cha ana omwe munthu akufuna kukhala nawo. Msilamu kuchita zimenezi popanda chifukwa chovomerezeka, ndi kusemphana ndi malamulo a Chisilamu. Chifukwa munthu...
by Ibn Muwahhid | Mar 27, 2019 | Zakaat
(Olemba: Ibn Muwahhid) Monga tinakambila mu gawo loyamba muja kuti Zakaat simangopelekedwa kwa aliyense koma pali anthu special omwe ali pa list yolandira zakaat. Allah anaikiratu list limenelo motere: إِنَّمَا الصَّدَقَاتُ لِلْفُقَرَاءِ وَالْمَسَاكِينِ...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Fiqh, Zakaat
Nisaab ya Zakaat za mbewu ndi zomera: Kapelekedwe ka zakaat za mbewu zimenezi. Pambuyo poti taona kuti ndimitundu iti ya mbewu yomwe Allah walamula kupereka Zakaat, ndipo tapeza kuti chimanga komaso mpunga mpira mawere ndi zina zomwe ambiri timalima kuno ku mudzi zili...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Zakaat
Tsopano tikhala tikuona gawo lachiwiri la Zakaat ya ulimi womwe ndi ulimi wa mbewu ndi zomera. Nnenemu tiona kuti ndi zomera ziti zomwe tikuyenera kupereka Zakaat. Tinamaliza kuwona Zakaat ya mbuzi, nkhosa komaso ng’ombe ngati ziweto zomwe amalawi timakhala nazo...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Fiqh
Mugawo ili tilongosola zinthu izi: 1. Zakaat ya ulimi 2. Mbuzi zomwe ziyenera kuperekedwa Zakaat Pambuyo poti tamaliza kuona zakaat ya ndalama komanso ya business ndipo takamba bwinobwino ndi maumboni komanso zitsanzo za kaperekedwe kake, tiyeni tipitirize gawo lina...
Your Comments