by Admin | Nov 4, 2019 | Fatawa, Featured
Fodya ndi chimodzi mwa zinthu zomwe zangobwera posachedwapa ndipo mbuyomu kunalibe. Nthawi ya Mtumiki salla Allah alaih wasallam kunalibe kugwiritsa ntchito fodya, komanso mbuyo mwakemo nthawi ya Atumiki onse kunalibe. Nthawi ya ma Shawabanso kunalibe fodya,...
by Admin | Jul 19, 2019 | Fatawa
The essential features of Friday Khutbah are the following according to the Sunnah of the Prophet -peace be upon him. The Imam should be in Wudu and should be properly dressed. It should be given from a pulpit (minbar). According to the Sunnah the minbar should be...
by Admin | Jul 19, 2019 | Fatawa
It may first seem logical that every Muslim should pray through his own mother language, so that he may understand what he says; but through a little more thinking and study, we shall find that there are strong arguments in favor of only one common language and that...
by Admin | Jul 2, 2019 | Fatawa
Funso: Ma Sheikh ena akaitanidwa kuti athandize odwala amabwera awiri, ndipo mmodzi akamasomera odwalayo winayo amakhala pambalipa ndikumaonetsa ma action ena ake, monga kumangoyasamula, kumangoziongola basi manjawa kumapanga zinazake, mkumakhala ngati...
by Admin | Jul 2, 2019 | Fatawa
Funso: Pali mtsikana yemwe sakudwala kumwezi koma kumayambiliroko ankadwala. Panopa almost two years ikutha osadwala. Sanagonepo ndi munthu chibadwire. Ndiye ali ndi vuto lakumva kuwawa mmimba ndi msana, koma kuchipatala anauzidwa kuti ngati akufuna kuti...
by Admin | Jul 2, 2019 | Fatawa
Funso: Ena chifukwa cha kuopa kukhala osakwatira kapena osakwatiwa, mapeto ake amakwatira munjira yosakhala bwino kapenanso kukwatira mkazi/mwamuna yemwe amanena kuti “zimenezo (myambo ya Chisilamu) ine sindingakwanitse” koma iwe ukumukwatirabe poopa kuti...
Your Comments