Magulu Ena a mu Chisilamu

Magulu Ena a mu Chisilamu

وَأَنَّ هَذَا صِرَاطِي مُسْتَقِيمًا فَاتَّبِعُوهُ وَلَا تَتَّبِعُوا السُّبُلَ فَتَفَرَّقَ بِكُمْ عَنْ سَبِيلِهِ ذَلِكُمْ وَصَّاكُمْ بِهِ لَعَلَّكُمْ تَتَّقُونَ  سورة الأنعام 153 (Auze kuti) ndithu, iyi ndi njira yanga yoongoka. Choncho itsateni. Ndipo musatsate njira...
Nkhani ya Mneneri Nooh (Noah) mtendere ukhale pa iye

Nkhani ya Mneneri Nooh (Noah) mtendere ukhale pa iye

Olemba: Sheikh Qullab T Jim Mneneri Nuhu (Nowa) ndi Mneneri wachiwiri kutumizidwa padziko lapansi pambuyo pa Mneneri Adam mwa Aneneri onse omwe Allah anawatumiza kwa anthu ndi cholinga chowawongelera ku njira yowongoka powayitanira iwo ku umodzi wa Mulungu (Tauhid),...
Imfa ya Munthu Okhulupilira ndi Osakhulupilira

Imfa ya Munthu Okhulupilira ndi Osakhulupilira

Nkhani inachokera kwa al-Bara’ ibn ‘Aazib yemwe anati: “tinapita ndi Mtumiki (Mtendere ndi Madalitso zipite kwa Iye) kumwambo woika mmanda mmodzi wa ma Ansar (mzika ya mumzinda wa Madina), ndipo titafika pa manda, tinapeza kuti sadaikidwe ku mphanga la manda. Kenako...
Imaan – Chikhulupiliro

Imaan – Chikhulupiliro

Imaan – الإيمان ​Imaan (chikhulupiliro) yeniyeni sichinthu chophweka kuchipeza. Imaan yomwe sivuta kuipeza ndi imene imapezeka kudzera mu nkhani zopeka. Munthu akhonza kukhala ndi imaan pa zinthu zabodza ndikumalimbikira ibaadah yake, koma kuchokera mu...
This Ummah will Divide into 73 Sects

This Ummah will Divide into 73 Sects

Imām al-Barbahārī (V died 329 AH) stated: “Know that Allah’s Messenger (H) said: “My ummah will divide into 73 sects, all of them will be in the Fire except for one, and that is the Jamā’ah.” It was said,“And who are they, O Allah’s Messenger?” He responded, “That...
Take the Qur’an

Take the Qur’an

A wealthy man and his son loved to collect rare works of art. They had everything in their collection, from Picasso to Raphael. They would often sit together and admire the great works of art. When the Vietnam conflict broke out, the son went to war. He was very...