by Admin | May 25, 2022 | Featured, Role Models, Shia
Ma Shia amamunena Mai wathu Wolemekezeka Aisha radhia Allahu anha kuti ndi munaafiq, komanso ndi wachimasomaso. Kuwonjezera pamenepo, m’mabuku mwawo akamamutchula mkazi wa Mtumiki aliyense amamutchula kuti Ummul Mu’mineena mkazi wa Mtumiki alaiha Ssalaam,...
by Admin | May 24, 2022 | Featured, Islam, Prophets
A TURNING POINT IN THE HISTORY OF ISLAM. Abdulkarim Shuaib May 20, 2022 02:56AM (Source: Book of Seerah ibn Hisham and Arab news 2012 religion article) The incident of Hudaibiyah reserves in history a significant phase of Islam when Muslims got an opportunity to...
by Admin | May 22, 2022 | Featured, Shia
Bodza la Mashia lonena kuti pali umboni woti Ali radhia Allahu anhu ndi Khalifa woyamba osati Abu Bakr radhia Allahu anhu 185- حتى لا ننخدع حقيقة الشيعة Pamene ma Swahaba wonse anagwirizana za utsogoleri komanso ulowammalo wa Abu Bakr, ‘Umar, ‘Uthman, kenako Ali...
by Admin | May 22, 2022 | Featured, Shia
Idris Al Maghribi anali Msilamu waku Morocco ndipo atakumana ndi da’wah ya ma Shia, anaganiza zosiya Chisilamu nkulowa Shia. Pa mwambo wa “kusinguka” (kutuluka mu chipembedzo china kuliwa mu chipembedzi china), pamene Yaasir Al Habib yemwe ndi mmodzi...
by Admin | May 22, 2022 | Featured, Shia
1. Chiphunzitso cha chi Shia chimanena kuti “Aah” ndilimodzi mwa maina a Allah. Umboni: Ma’anil Akhbaar, chitabu cholembedwa ndi Al Qummi, page 304: Onani chithunzi 2. Ma Shia amakhulupilira kuti Abu Talib (Malume a Mtumiki), Abdullah ndi Aaminah (Makolo a...
Your Comments