by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Zakaat
Tsopano tikhala tikuona gawo lachiwiri la Zakaat ya ulimi womwe ndi ulimi wa mbewu ndi zomera. Nnenemu tiona kuti ndi zomera ziti zomwe tikuyenera kupereka Zakaat. Tinamaliza kuwona Zakaat ya mbuzi, nkhosa komaso ng’ombe ngati ziweto zomwe amalawi timakhala nazo...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Fiqh
Mugawo ili tilongosola zinthu izi: 1. Zakaat ya ulimi 2. Mbuzi zomwe ziyenera kuperekedwa Zakaat Pambuyo poti tamaliza kuona zakaat ya ndalama komanso ya business ndipo takamba bwinobwino ndi maumboni komanso zitsanzo za kaperekedwe kake, tiyeni tipitirize gawo lina...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Fiqh
In shaa Allah tiona za kaperekedwe ka Zakaat pa business yopanga rent katundu monga nyumba magalimoto komanso malo. Mugawo lomwe lapita tinakamba za kaperekedwe ka Zakaat pa ma business omwe tinawatchula kuti business wamba. Komanso business yomagulitsa ma galimoto,...
by Ibn Muwahhid | Feb 21, 2019 | Fiqh, Zakaat
Pambuyo pa kuona za kapelekedwe ndi kaonkhetsedwe ka Zakaat ya ndalama, in shaa Allah tiona za kawelengedwe ndi kaonkhetsedwe ka Zakaat pa business. Ndipo tikhala tiona mbali izi 1. Zakaat ya business wamba ochulukawa. 2. Zakati pa nyumba ndi malo kapenaso ma galimoto...
by Ibn Muwahhid | Jan 23, 2019 | Fiqh, Zakaat
(Olemba: Ibn Muwahhid) 1. Anthu omwe ali oyenela kupeleka Zakaat 2. Anthu omwe akuyenela kulandila Zakaat. Monga tinafotokozera pa tanthauzo pa Zakaat lija (mutha kuona gawo loyambilira) zinaonetselatu kuti si munthu aliyense amene angapeleke zakaat ayi. Zakaat ndi...
Your Comments