by Kuunikira | May 24, 2022 | Fatawa, Featured, Kuunikira, Marriage, Sunnah
Tisaiwale kukumbukira kuti Kusangalala tsiku la Nikkah, sikuti Ndi chikakamizo ayi, koma kuti ndi Sunnah, chifukwa Anthu amazikakamiza ndikupanikizika Poona kuti afune asafune akuyenera kuchititsa Chisangalalo cha Nikkah yawo,dziwani kuti Kumangitsa Nikkah ndi chinthu...
by Kuunikira | May 24, 2022 | Featured, Kuunikira
Pakukhala kuti Chisilamu chidaunikira mbali zonse za umoyo, Mu Qur’an ndi Mahadith (zoyankhula za mtumiki). Ndipo masahabah Adagwira ntchito yotamandika yotulutsa khokwe za maphunziro kuchokera mu Qur’an ndi Mahadith, pambuyo pawo padabweraso Ma Imam ndi...
by Kuunikira | May 23, 2022 | Featured, Kuunikira
Wapita mwezi wa madalitso, Mwezi wa mapemphero, mwezi wa Qur’an, mwezi opeleka Chopeleka, Mwezi ochulukitsa zabwino, wapita basi mwezi umene oluza aluza opambana apambana, apambana amene adasala mwa chikhulupiliro natsatira ziphuzitso za Sharia zakusala,...
by Kuunikira | May 23, 2022 | Featured, Kuunikira
“Akalowa bwanji ku ng’anjo ya moto akadaulo, akatswiri komanso anthu ena amene anachita ndi kugwira ntchito zopambana, ndizopititsa patsogolo umoyo wa anthu pa dziko lino lapansi?. – Anthu okanira amene anagwira ntchito yotamandika pa dziko lapansi,...
Your Comments