Ma Shia amamunena Mai wathu Wolemekezeka Aisha radhia Allahu anha kuti ndi munaafiq, komanso ndi wachimasomaso.
Kuwonjezera pamenepo, m’mabuku mwawo akamamutchula mkazi wa Mtumiki aliyense amamutchula kuti Ummul Mu’mineena mkazi wa Mtumiki alaiha Ssalaam, pomwe Aisha radhia Allahu anha amangomutchula dzina lake basi (Aisha bint Abi Bakr), komanso amawonjezera kumapetoko mawu otembelera oti: “la’natullahi alaihima (thembelero la Allah lipite kwa Aisha ndi bambo ake)” mmalo mwa “radhiallahu anhuma (Allah asangalale nawo)”.
Bodza limenelitu analifalitsa kwambiri ndi mtsogoleri wa ma munaafiq Abdullah bun Ubayya bun Salool. Koma ngakhale kuti Allah anaitsutsa nkhaniyi ndi kuyiwonetsera kuti ndiyabodza, ma Shia sanafune kumvera Allah komanso sanamukhulupilire, koma iwo anasankha kumvera munaafiq ameneyu.
Tidziwe kuti aliyense yemwe amamunyoza mkazi wolemekezeka wa Mtumiki munjira iliyonse, ameneyo ndi kaafir.
Makamakatu iwo amatenganso kankhani kabodza kaja kamene ananamiziridwa Aisha radhia Allahu anha kuti anachita chiwerewere ndi munthu wina yemwe anagonereza pamene Aaisha anasochera ndipo munthuyo anamuthandiza pomulondolera njira.
Alhamdulillah Allah anatilongosolera mu Qur’an yathu (anzathuwo paja akuti alibe Qur’an), ndipo ife tinakhulupilira. N’chifukwa chake ma ulamaa athu olemekezeka onse anagwirizana kuti aliyense yemwe angamunamizire Mai wa Okhulupilira Aisha radhia Allahu anha zankhani yopeka imeneyi, ndithu ameneyo ndi kaafir mopanda kuchotsera, chifukwa akukanira zomwe Allah analongosola potsutsa za nkhaniyi, ndipo akutsutsa ma Aaya 10 omwe adadza pankhaniyi. Kaafir.
Ukafir wakensotu wa aja opembedza mafano, osati nkukhalanso Msilamu ayi.
Koma kodi anthu amenewa akamayankhula zonyoza Mkazi wolemekezeka wa Mtumiki, zikutanthauza chani?
– zikutanthauza kuti Mtumiki anali wopelewera mu utumiki wake chifukwa choti anakwatira munaafiq.
Choncho anthu amenewa kuti apulumuke kuchilango cha Allah, akuyenera kutawubitsidwa, ndipo yemwe wakana kupanga tawba akuyenera kuphedwa; mtembo wakewo uponyedwe mzenje – asapangiridwe mwambo wa jeneza monga kusambitsidwa, kuvekedwa ndi kuswalitsidwa. Komanso pasapezeke dua iliyonse yompangira kaafir ameneyo .. amenewo ndi malipiro amunthu wotuluka Chisilamu.
Your Comments