by Admin | Jul 17, 2020 | Featured, Islam
Tikudziwa bwinolomwe kuti ena mwa majinn ndi ma shaytwaan (asatana), amenewa ndi ma jinn oipa, ndipo asatanawa amafa mmene amafera majinn ndi anthu. Onsewa akulowa mukuyankhula kwa Allah Ta’ala koti: كُلُّ مَنْ عَلَيْهَا فَانٍ – وَيَبْقَى وَجْهُ رَبِّكَ...
by Admin | Feb 16, 2020 | Featured, Islam
Funso: Kodi nchifukwa chani anthu amakonda kufunsa kuti “ndikufunafuna Sheikh omwe amachotsa ziwanda, amene ali ndi number yawo anditumizire?” Yankho: Amafuna kuti akawawelengere Qur’an, ma Dua ndi ma Dhikr chifukwa iwowo sadziwa, komanso safuna...
by Admin | May 15, 2019 | Fasting
Timamva kuti shaytwaan amamangidwa mwezi wa Ramadhan, kodi ruqya yochotsa ziwanda ndiyololedwa kupanga mwezi wa Ramadhan? Ngati zili zololedwa, ziwanda zingapezeke bwanji? Ruqya ndiyololedwa kupanga nthawi iriyonse, tsiku lirilonse komanso mwezi uliwonse. Palibe...
Your Comments