Zakaat ya Ndalana – Nisaab

Mu gawo lapita lija taona Nisaab ya ndalama komaso ndalama zomwe umafunika kupereka ngati ndalama zokwana pa Nisaab zazungulira chaka. Mmene tinaonela muja, Nisaab imapezeka kuti ndi MK 221,000 potengera nisaab ya siliva. Zomwe zimaonetsa kuti anthu ambiri tili mu...

Zakaat ya Ndalama

Kapelekedwe ka Zakaat ya ndalama. Kodi Nisaab ya ndalama ndi zingati? Chaka chimazungulira bwanji pa Zakaat za ndalama? Ndi ndalama zingati zomwe umapeleka pa ndalama yomwe ulinayo? Tinalongosola mu chigawo chapita kuti Zakaat ya ndalama imachokera pa golide komaso...

Chuma Chopelekera Zakaat

(Olemba: Ibn Muwahhid) Chuma chomwe timapelekera Zakaat tutha kuchigawa patatu. 1. Ndalama 2. Katundu 3. Za ulimi Tiyamba kuona gulu lilironse bwinobwino kuti ndiziti zomwe ziperekedwe mmagawo amenewa 1. Ndalama Ndalama zomwe munthu uli nazo zimayenera kuperekedwa...

Oyenera Kulandira Zakaat

(Olemba: Ibn Muwahhid) Monga tinakambila mu gawo loyamba muja kuti Zakaat simangopelekedwa kwa aliyense koma pali anthu special omwe ali pa list yolandira zakaat. Allah anaikiratu list limenelo motere: إِنَّمَا الصَّدَقَاتُ لِلْفُقَرَاءِ وَالْمَسَاكِينِ...
Zakaat ya Mbewu (1)

Zakaat ya Mbewu (1)

Nisaab ya Zakaat za mbewu ndi zomera: Kapelekedwe ka zakaat za mbewu zimenezi. Pambuyo poti taona kuti ndimitundu iti ya mbewu yomwe Allah walamula kupereka Zakaat, ndipo tapeza kuti chimanga komaso mpunga mpira mawere ndi zina zomwe ambiri timalima kuno ku mudzi zili...