Mkazi Kugwira Ntchito Mchisilamu

Mkazi Kugwira Ntchito Mchisilamu

Mkazi ndiwololedwa kugwira ntchito. Koma pali zingapo zofunika kutsatira komanso zina zofunika kupewa. Pachiyambi penipeni, tiona shari’ah, ndipo tisiye zomwe society imafuna. Mkazi ndimunthu amene amayenera kukhala panyumba, kusamalira m’nyumba, ana...