Kuvala Hijaab ndi Zolinga zake Mchisilamu

بسمِ الله الرحمن الرحيم KUVALA HIJAB NDI ZOLINGA ZAKE MCHISILAMU Uwu ndi uthenga kwazichemwali athu a Chisilamu.Alhamdulilah kuti Masiku ano Hijab ili paliponse limodzi ndi kutsogola kwa ma company opanga Zovala makamaka mikanjo yazimayi.kuli Mitundu Yochuluka ya...

Bridal Shower Mchisilamu

Liwu loti “Bridal” (bride to be) likuimira mkazi yemwe ali ndi ukwati wake posachedwa. “Shower” ndi kupereka mwambo ndi mphatso komanso madalitso ndi malangizo ndi kumukondwelera pamene azikakhala m’banja ndi mwamuna wake.   Malingana ndi...

Mavalidwe a pa Nikaah ndi pa Walimah

Kusiyana kwa veil ndi wedding dress Ma Sheikh odalirika pamaphunziro a Chisilamu akhala akuchilimika kuletsa chovala chija chotchedwa “veil” pa nikaah. Lero tikufuna tichitirepo chidwi ndi kufotokoza momveka bwino pa nkhani imeneyi kuti aliyense atenge choonadi cha...

Walimah (Chisangalalo Pambuyo pa Nikaah)

Walimah ndi phwando kapena chisangalalo chomwe chimabwera kumapeto komangitsa banja (Nikaah). Ndizololedwa kuchita walimah nthawi yomweyo kapena kuchedwetsa malingana ndi kuthekera kwa munthu, ndipo iyenera kuchitika munjira yomwe ili yololedwa ndi malamulo a...

Mafunsidwe a Mahr

Zomwe zimachitika masiku ano zobisa mahr nkudzaitanitsa nthawi yomwe nikaah ikuchitika, si chiphunzitso cha Chisilamu, komanso mboni ziwiri kufunsa mahr tsiku la nikaah sichiphunzitso cha Chisilamu. Mahr imayenera kukhala ikudziwika kwa waliyy (muyang’aniri wa mkazi)...