Uzair

Uzair anali munthu woyera komanso wanzeru. Anakhala pambuyo pa Mneneri Sulaiman alaih salaam komanso asanabwere Mneneri Zakaria alaih salaam. Tsiku lina monga mwachizolowezi chake, Mneneri anakayendera munda wake pa bulu. Chakumasana, anafika pa kamzinda kena...