by Admin | Jun 28, 2019 | Role Models
Mbiri ya ‘Uthmaan bun ‘Affaan mwachidule Alongosolereni ana anu achichepere nkhani zimenezi Uthman bun Affaan radhia Allah anhu anabadwa patadutsa zaka 7 chibadwire Mtumiki salla Allah alaih wasalaam. Iye anali ochokera mu nthambi ya fuko la Quraysh...
Your Comments