Tiyidziwe Masjid Al Aqsa Yeniyeni

Ndizofunika Kwa Msilamu Aliyense Kudziwa Kusiyana Kwa Masjidul Aqsa Ndi Masjid Qubbat Assakharah. Kuyambira kalekale kwambiri, Masjidul Aqsa ku Palestine yakhala ikukumana ndi zipsinjo zambiri kuchokera kwa adani a Chisilamu omwe safuna kuona Chisilamu chikufalikira...

‘Umar bun Al-Khattwaab (Al-Faaruq)

Mbiri ya Umar bun Al-Khattwaab mwachidule Alongosolereni ana anu achichepere nkhani zimenezi Umar bun Al Khattaab radhia Allah anhu anali mmodzi mwa ma Khalifa amphamvu komanso opambana, ochokera m’banja la Bani ‘Adiy, fuko la Quraysh ku Makkah. Anali...