Kukhala ndi Munthu Osiya Chisilamu

Kukhala ndi Munthu Osiya Chisilamu

Funso: “Mwamuna achoke muchipembedzo chake cha Chisilamu mkumtsatira muchipembedzo chake (ndikhulupilira mukutanthauza kumtsatira mkazi). Ndafunsa funsoli chifukwa ndakhala ndikuona ambiri kuno ku Joni akupanga zimenezo akuti chifukwa chofuna kukhala mwa...
Kuopsa kwa Kumpanga Msilamu Kaafir Popanda Umboni

Kuopsa kwa Kumpanga Msilamu Kaafir Popanda Umboni

 الفتاوى الشرعية في القضايا العصرية #ص٨٢-٨٥ Fatawa Al Shar’iyya fil Qadhaayal ‘Asriya Page 82-85 “Kumuchita munthu kaafir yemwe ali osayenera kumuchita kaafir sizololedwa. Amene akuyenera kumuchita kaafir ndi amene ali oyenera kumuchita kaafir. Amene...